1 Mbiri 26:14 BL92

14 Ndi maere a kum'mawa anagwera Selemiya. Ndipo anacitira maere Zekariya mwana wace, phungu wanzeru, ndi maere anamgwera kumpoto;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 26

Onani 1 Mbiri 26:14 nkhani