1 Mbiri 26:20 BL92

20 Ndipo wa Alevi, Ahiya anayang'anira cuma ca nyumba ya Mulungu, ndi cuma ca zopatulika.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 26

Onani 1 Mbiri 26:20 nkhani