1 Mbiri 26:28 BL92

28 Ndipo zonse adazipatula Samueli mlauli, ndi Sauli mwana wa Kisi, ndi Abineri mwana wa Neri, ndi Yoabu mwana wa Zeruya; ali yense anapatula kanthu kali konse, anazisunga Selomoti ndi abale ace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 26

Onani 1 Mbiri 26:28 nkhani