1 Mbiri 26:4 BL92

4 Ndipo Obedi Edomu anali nao ana, woyamba Semaya, waciwiri Yozabadi, wacitatu Yowa, wacinai Sakara, wacisanu Netaneli,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 26

Onani 1 Mbiri 26:4 nkhani