1 Mbiri 26:6 BL92

6 Kwa Semaya mwana wace yemwe kunabadwa ana, akulamulira nyumba ya atate wao; pakuti anali ngwazi zamphamvu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 26

Onani 1 Mbiri 26:6 nkhani