1 Mbiri 26:8 BL92

8 Onsewa ndiwo a ana a Obedi Edomu; iwo ndi ana ao, ndi abale ao, anthu odziwa mphamvu yakutumikira, makumi asanu ndi limodzi mphambu awiri a Obedi Edomu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 26

Onani 1 Mbiri 26:8 nkhani