11 Wacisanu ndi citatu wa mwezi wacisanu ndi citatu ndiye Sibekai Mhusati wa Afera; ndi m'cigawo mwace zikwi makumi awiri mphambu zinai.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 27
Onani 1 Mbiri 27:11 nkhani