1 Mbiri 27:14 BL92

14 Wakhumi ndi cimodzi wa mwezi wakhumi ndi cimodzi ndiye Benaya Mpiratoni wa ana a Efraimu; ndi m'cigawo mwace zikwi makumi awiri mphambu zinai.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 27

Onani 1 Mbiri 27:14 nkhani