1 Mbiri 27:5 BL92

5 Kazembe wacitatu wa khamu wa mwezi wacitatu ndiye Benaya mwana wa Yehoyada wansembe wamkuru; ndi m'cigawo mwacemunalinso zikwi makumi awiri mphambu zinai.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 27

Onani 1 Mbiri 27:5 nkhani