1 Mbiri 27:7 BL92

7 Wacinai wa mwezi wacinai ndiye Asebeli mbale wa Yoabu, ndi pambuyo pace Zebadiya mwana wace; ndi m'cigawo mwace munali zikwi makumi awiri mphambu zinai.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 27

Onani 1 Mbiri 27:7 nkhani