1 Mbiri 28:14 BL92

14 ca golidi woyesedwa kulemera kwace wa zipangizo zagolidi, wa zipangizo zonse za nchito ya mtundu uli wonse; ca siliva wa zipangizo zasiliva woyesedwa kulemera kwace, wa zipangizo za nchito ya mitundu mitundu;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 28

Onani 1 Mbiri 28:14 nkhani