1 Mbiri 28:20 BL92

20 Ndipo Davide anati kwa Solomo mwana wace, Limbika, nulimbe mtima, nucicite; usaopa, kapena kutenga nkhawa; pakuti Yehova Mulungu, ndiye Mulungu wanga, ali nawe; sadzakusowa kapena kukutaya mpaka zitatha nchito zonse za utumiki wa nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 28

Onani 1 Mbiri 28:20 nkhani