1 Mbiri 29:12 BL92

12 Zolemera ndi ulemu zifuma kwanu, ndipo mucita ufumu pa zonse, ndi m'dzanja mwanu muli mphamvu yaikuru; kukuza ndi kupatsa onse mphamvu kuli m'dzanja lanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:12 nkhani