1 Mbiri 29:25 BL92

25 Ndipo Yehova anakuza Solomo kwakukuru pamaso pa Aisrayeli onse, nampatsa ulemerero wacifumu, wakuti, asanakhale iyeyu, panalibe mfumu ya Israyeli inali nao wotero.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:25 nkhani