1 Mbiri 29:27 BL92

27 Ndipo nthawi yoti anakhala mfumu ya Israyeli ndiyo zaka makumi anai; zaka zisanu ndi ziwiri anakhala mfumu m'Hebroni, ndi zaka makumi atatu anakhala mfumu m'Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:27 nkhani