1 Mbiri 29:29 BL92

29 Zocita mfumu Davide tsono, zoyamba ndi zotsiriza, taonani, zalembedwa m'buku la mau a Samueli mlauli, ndi m'buku la mau a Natani mneneri, ndi m'buku la mau a Gadi mlauli;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:29 nkhani