1 Mbiri 29:3 BL92

3 Ndiponso popeza ndikondwera nayo nyumba ya Mulungu wanga, cuma cangacanga ca golidi ndi siliva ndiri naco ndicipereka ku nyumba ya Mulungu wanga, moenjezera ndi zonse ndazikonzeratu nyumba yopatulikayo;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:3 nkhani