16 Ndi ana a Yehoyakimu: Yekoniya mwana wace, Zedekiya mwana wace.
17 Ndi mwana wa Yekoniya: Asiri, Sealitiyeli mwana wace,
18 ndi Malikiramu, ndi Pedaya, ndi Senazara, Yekamiya, Hosama, Nedabiya.
19 Ndi ana a Pedaya: Zerubabeli, ndi Simei; ndi ana a Zerubabeli: Mesulamu, ndi Hananiya; ndipo Selomiti ndiye mlongo wao,
20 ndi Hasuba, ndi Oheli, ndi Berekiya, ndi Hasadiya, ndi Yusabi-hesedi; asanu.
21 Ndi ana a Hananiya: Pelatiya, ndi Yesaya, ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya, ana a Sekaniya.
22 Ndi mwana wa Sekaniya: Semaya; ndi ana a Semaya: Hatusi, ndi Igali, ndi Bariya, ndi Neariya, ndi Safati; asanu ndi mmodzi.