1 Mbiri 4:21 BL92

21 Ana a Sela mwana wa Yuda: Eri atate wa Leka, ndi Laada atate wa Maresa, ndi mabanja a nyumba ya iwo oomba bafuta wa thonje losansitsa a nyumba ya Asibeya,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 4

Onani 1 Mbiri 4:21 nkhani