16 Ndipo anakhala m'Gileadi m'Basana, ndi m'midzi yace, ndi podyetsa pace ponse pa Saroni, mpaka malire ao.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 5
Onani 1 Mbiri 5:16 nkhani