25 Koma analakwira Mulungu wa makolo ao, nacita cigololo, ndi kutsata milungu ya mitundu ya anthu a m'dziko, amene Mulungu adaononga pamaso pao.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 5
Onani 1 Mbiri 5:25 nkhani