32 Ndipo anatumikira ndi kuyimba pakhomo pa kacisi wa cihema cokomanako mpaka Solomo adamanga nyumba ya Yehova m'Yerusalemu, naimirira m'utumiki wao monga mwa malongosoledwe ao.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 6
Onani 1 Mbiri 6:32 nkhani