60 ndi ku pfuko la Benjamini Geba ndi mabusa ace, ndi Alemeti ndi mabusa ace, ndi Anatoti ndi mabusa ace. Midzi yao yonse mwa mabanja ao ndiyo midzi khumi ndi itatu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 6
Onani 1 Mbiri 6:60 nkhani