71 Ana a Gerisomu analandira motapa pa mabanja a pfuko la Manase logawika pakati, Golani m'Basana ndi mabusa ace, ndi Asitaroti ndi mabusa ace;
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 6
Onani 1 Mbiri 6:71 nkhani