1 Mbiri 7:11 BL92

11 Onsewa ndiwo ana a Yedyaeli; ndiwo akuru a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu zikwi khumi mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana awiri akuturuka kugulu kunkhondo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 7

Onani 1 Mbiri 7:11 nkhani