1 Mbiri 7:15 BL92

15 ndi Makiri anadzitengera mkazi, mlongo wace wa Hupimu ndi Supimu, dzina lace ndiye Maaka. Ndipo dzina la mwana waciwiri wa Manase ndiye Tselofekadi. Ndi Tselofekadi anali ndi ana akazi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 7

Onani 1 Mbiri 7:15 nkhani