1 Mbiri 7:21 BL92

21 ndi Zabadi mwana wace, ndi Sutela mwana wace, ndi Ezeri, ndi Eleadi, amene anthu a Gadi obadwa m'dziko anamupha, popeza anatsikira kukalanda zoweta zao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 7

Onani 1 Mbiri 7:21 nkhani