28 Ndipo dziko lao, ndi pokhala pao ndizo Beteli ndi miraga yace, ndi kum'mawa Narani, ndi kumadzulo Gezeri ndi miraga yace, ndi Sekemu ndi miraga yace, mpaka Aza ndi miraga yace;
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 7
Onani 1 Mbiri 7:28 nkhani