1 Mbiri 7:7 BL92

7 Ndi ana a Bela: Ezboni, ndi Uzi, ndi Uzieli, ndi Yerimoti, ndi hi, asanu; akuru a nyumba za makolo ao, ngwazi zamphamvu, owerengedwa m'mabuku a cibadwidwe zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza makumi atatu ndi anai.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 7

Onani 1 Mbiri 7:7 nkhani