1 Mbiri 9:13 BL92

13 ndi abale ao, akuru a nyumba za makolo ao cikwi cimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi limodzi, anthu odziwitsitsa Debito ya utumiki wa nyumba ya Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 9

Onani 1 Mbiri 9:13 nkhani