1 Mbiri 9:29 BL92

29 Ndi ena a iwo anaikidwa ayang'anire zipangizo ziti zonse, ndi zipangizo zonse za malo opatulika, ndi ufa wosalala, ndi vinyo, ndi mafuta, ndi libano, ndi zonunkhira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 9

Onani 1 Mbiri 9:29 nkhani