1 Mbiri 9:31 BL92

31 Ndi Matitiya wina wa Alevi, ndiye mwana woyamba wa Salumu Mkora, anaikidwa ayang'anire zokazingidwa m'ziwaya.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 9

Onani 1 Mbiri 9:31 nkhani