19 Ndipo iwo anauka mamawa, nalambira pamaso pa Yehova, nabwerera, nafikanso kwao ku Rama; ndipo Elikana anadziwa mkazi wace Hana, Yehova namkumbukila iye.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1
Onani 1 Samueli 1:19 nkhani