20 Ndipo panali pamene nthawi yace inafika, Hana anaima, nabala mwana wamwamuna: namucha dzina lace Samueli, nati, Cifukwa ndinampempha kwa Yehova,
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1
Onani 1 Samueli 1:20 nkhani