21 Ndipo munthuyo Elikana, ndi a pa banja lace onse, anakwera kukapereka kwa Yehova nsembe ya caka ndi caka, ndi ya cowinda cace.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1
Onani 1 Samueli 1:21 nkhani