1 Samueli 1:24 BL92

24 Ndipo atamletsa kuyamwa anakwera naye, pamodzi ndi ng'ombe ya zaka zitatu, ndi efa wa ufa, ndi thumba la vinyo, nafika naye ku nyumba ya Yehova ku Silo; koma mwanayo anali wamng'ono.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1

Onani 1 Samueli 1:24 nkhani