4 Ndipo pofika tsiku lakuti Elikana akapereka nsembe, iye anapatsa Penina mkazi wace, ndi ana ace onse, amuna ndi akazi, gawo lao;
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1
Onani 1 Samueli 1:4 nkhani