8 Ndipo mwamuna wace Elikana anati kwa iye, Hana, umaliriranji? ndipo umakaniranji kudya? ndipo mtima wako uwawa ninji? Ine sindiri wakuposa ana khumi kwa iwe kodi?
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1
Onani 1 Samueli 1:8 nkhani