1 Samueli 1:9 BL92

9 Comweco Hana anauka atadya m'Silo, ndi kumwa. Ndipo Eli wansembeyo anakhala pa mpando wace pa mphuthu ya Kacisi wa Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1

Onani 1 Samueli 1:9 nkhani