1 Samueli 11:2 BL92

2 Ndipo Nahasi Mamoni ananena nao, Ndidzapangana nanu, ngati mulola kuti maso a ku dzanja lamanja anu onse akolowoledwe; potero ndidzanyazitsa Aisrayeli onse.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 11

Onani 1 Samueli 11:2 nkhani