9 Ndipo anati kwa mithenga inadzayi, Muzitero kwa anthu a ku Yabezi Gileadi, Mawa litatentha dzuwa, mudzaona cipulumutso. Ndipo mithenga inadza niuza a ku Yabezi; nakondwara iwowa.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 11
Onani 1 Samueli 11:9 nkhani