1 Samueli 12:12 BL92

12 Ndipo pamene munaona kuti Nahasi mfumu ya ana a Amoni inadza kuponyana nanu, munanena ndi ine, Koma mfumu itiweruze; ngakhale mfumu yanu ndiye Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12

Onani 1 Samueli 12:12 nkhani