15 Koma mukapanda kumvera mau a Yehova, ndi kupikisana ndi lamulo la Yehova, dzanja la Yehova lidzatsutsana nanu, monga linatsutsana ndi makolo anu.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12
Onani 1 Samueli 12:15 nkhani