1 Samueli 12:19 BL92

19 Ndipo anthu onse ananena ndi Samueli, Mupempherere akapolo anu kwa Yehova Mulungu wanu, kuti tingafe; popeza pamwamba pa zoipa zathu zonse tinaonjeza coipa ici, cakuti tinadzipemphera mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12

Onani 1 Samueli 12:19 nkhani