1 Samueli 12:20 BL92

20 Ndipo Samueli ananena kwa anthuwo, Musaope; munacitadi coipa ici conse, koma musaleka kutsata Yehova, koma mutumikire Yehova ndi mtima wanu wonse;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12

Onani 1 Samueli 12:20 nkhani