1 Samueli 13:11 BL92

11 Ndipo Samueli anati, Mwacitanji? Nati Sauli, Cifukwa ndinaona kuti anthuwo alinkubalalika kundisiya ine, ndi kuti inu simunafika masiku aja tinapangana, ndi kuti Afilisti anasonkhana ku Mikimasi;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:11 nkhani