1 Samueli 13:12 BL92

12 cifukwa cace ndinati, Afilisti adzatitsikira pane pa Giligala, ndisanapembedze Yehova; potero ndinadzifulumiza, ndi kupereka nsembe yopsereza.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:12 nkhani