1 Samueli 13:13 BL92

13 Ndipo Samueli ananena ndi Sauli, Munacita kopusa; simunasunga lamulo la Yehova Mulungu wanu, limene iye anakulamulirani; mwenzi Yehova atakhazikitsa nthawi yino ufumu wanu, ukhale pa Israyeli nthawi yosatha.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:13 nkhani