1 Samueli 13:14 BL92

14 Koma tsopano ufumu wanu sudzakhala cikhalire; Yehova wadzifunira munthu wa pamtima pace; ndipo Yehova wamuika iye akhale mtsogoleri wa anthu ace, cifukwa inu simunasunga cimene Yehova anakulamulirani.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:14 nkhani