1 Samueli 13:15 BL92

15 Ndipo Samueli anauka nacoka ku Giligala kunka ku Gibeya wa ku Benjamini. Ndipo Sauli anawerenga anthu amene anali naye, monga mazana asanu ndi limodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:15 nkhani